Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 23:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mneneri wokhala ndi loto, anene loto lace; ndi iye amene ali ndi mau anga, anene mau anga mokhulupirika. Kodi phesi ndi ciani polinganiza ndi tirigu? ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:28 nkhani