Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 23:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, ponenera abusa amene adyetsa anthu anga: Mwabalalitsa zoweta zanga, ndi kuzipitikitsa, ndipo simunazizonda; taonani, ndidzakusenzani inu kuipa kwa nchito zanu, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:2 nkhani