Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 22:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova atero za nyumba ya mfumu ya Yuda: Ndikuyesa iwe Gileadi, ndi mutu wa Lebano; koma ndidzakuyesa iwe cipululu, ndi midzi yosakhalamo anthu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22

Onani Yeremiya 22:6 nkhani