Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 22:29-30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

29. Iwe dziko, dziko, dziko lapansi, tamvera mau a Yehova.

30. Atero Yehova, Lembani munthu uyu wopanda ana, munthu wosaona phindu masiku ace; pakuti palibe munthu wa mbeu zace adzaona phindu, ndi kukhala pa mpando wacifumu wa Davide, ndi kulamuliranso m'Yuda.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 22