Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 21:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye amene akhala m'mudzi uwu adzafa ndi lupanga, ndi njala, ndi caola; koma iye amene aturuka, napandukira kwa Akasidi akuzinga inu, adzakhala ndi moyo, ndipo moyo wace udzapatsidwa kwa iye ngati cofunkha.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 21

Onani Yeremiya 21:9 nkhani