Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 21:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pambuyo pace, ati Yehova, ndidzapereka Zedekiya mfumu ya Yuda, ndi atumiki ace, ndi anthu, ngakhale a m'mudzi uwu amene asiyidwa ndi caola, ndi lupanga, ndi njala, m'dzanja la Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo, ndi m'dzanja la adani ao, ndi m'dzanja la amene afuna moyo wao; ndipo adzawakantha ndi lupanga lakuthwa; osawaleka, osacita cisoni, osacita cifundo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 21

Onani Yeremiya 21:7 nkhani