Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 21:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova, Mulungu wa Israyeli atero, Taonani, ndidzabweza zida za nkhondo zimene ziri m'manja anu, zimene mumenyana nazo ndi mfumu ya ku Babulo, ndi Akasidi akuzinga inu, kunja kwa malinga, ndipo ndidzazisonkhanitsa pakati pa mudzi uwu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 21

Onani Yeremiya 21:4 nkhani