Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 21:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, Ine ndine mdani wako, iwe wokhala m'cigwa, ndi pa thanthwe la m'cidikha, ati Yehova; inu amene muti, Ndani adzatsikira kumenyana ndi ife? ndani adzalowa m'zokhalamo zathu?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 21

Onani Yeremiya 21:13 nkhani