Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 2:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Osati, Ali kuti Yehova amene anatikweza kucokera ku dziko la Aigupto, natitsogolera m'cipululu, m'dziko loti se ndi la maenje, m'dziko la cirala ndi la mthunzi wa imfa, m'dziko losapitamo anthu, losamangamo anthu?

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 2

Onani Yeremiya 2:6 nkhani