Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 2:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pita nupfuule n'makutu a Yerusalemu, kuti, Yehova atero, Ndikumbukira za iwe kukoma mtima kwa ubwana wako, cikondi ca matomedwe ako; muja unanditsata m'cipululu m'dziko losabzya lamo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 2

Onani Yeremiya 2:2 nkhani