Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 2:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anthu anga anacita zoipa ziwiri; anandisiya Ine kasupe wa madzi amoyo, nadziboolera zitsime, zitsime zong'aluka, zosakhalamo madzi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 2

Onani Yeremiya 2:13 nkhani