Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 19:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzadyetsa iwo mnofu wa ana ao amuna ndi akazi, ndipo adzadya yense mnofu wa mbale wace, m'nkhondo yozinga ndi m'kupsinjikako, kumene adani ao, ndi iwo akufuna moyo wao, adzapsinja iwo nako.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 19

Onani Yeremiya 19:9 nkhani