Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 19:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzataya uphungu wa Yuda ndi wa Yerusalemu m'malo ano; ndipo ndidzagwetsa iwo ndi lupanga pamaso pa adani ao, ndi pa dzanja la iwo amene afuna moyo wao; mitembo yao ndidzapatsa ikhale cakudya ca mbalame za m'mlengalenga, ndi ca zirombo za dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 19

Onani Yeremiya 19:7 nkhani