Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 19:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli atero, Taonani, ndidzatengera mudzi uwu ndi midzi yace yonse coipa conse cimene ndaunenera; cifukwa anaumitsa khosi lao, kuti asamve mau anga.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 19

Onani Yeremiya 19:15 nkhani