Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 18:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nyumba ya Israyeli inu, kodi sindingathe kucita ndi inu monga woumba uyu? ati Yehova. Taonani, monga dothi m'dzanja la woumba, momwemo inu m'dzanja langa, nyumba ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 18

Onani Yeremiya 18:6 nkhani