Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace mupereke ana ao kunjala, mupereke iwo ku mphamvu ya lupanga; akazi ao akhale opanda ana, ndi amasiye; amuna ao aphedwe ndi imfa, ndi anyamata ao apandidwe ndi lupanga kunkhondo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 18

Onani Yeremiya 18:21 nkhani