Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 18:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anati, Tiyeni, tilingalire Yeremiya comcitira coipa; pakuti cilamulo sicidzathera wansembe, kapena uphungu wanzeru, kapena mau mneneri. Tiyeni, timpande iye ndi lilime, tisamvere iye mau ace ali onse.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 18

Onani Yeremiya 18:18 nkhani