Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 18:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsopano nenatu kwa anthu a Yuda, ndi kwa okhala m'Yerusalemu, kuti, Atero Yehova: Taonani, Ine ndipangira inu coipa, ndilingalira inu kanthu kakucitira inu coipa; mubwerere tsono inu nonse, yense ku njira yace yoipa, nimukonze njira zanu ndi macitidwe anu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 18

Onani Yeremiya 18:11 nkhani