Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 17:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzakhala ngati mtengo wooka kuti madzi, wotambalitsa mizu yace pamtsinje, wosaopa pofika nyengo yadzuwa, koma tsamba lace likhala laliwisi; ndipo subvutika cakaca cirala, suleka kubala zipatso.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17

Onani Yeremiya 17:8 nkhani