Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 17:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzacokera ku midzi ya Yuda, ndi ku malo akuzungulira Yerusalemu, ndi ku dziko la Benjamini, ndi kucidikha, ndi kumapiri, ndi ku Mwela, ndi kudza nazo nsembe zopsereza, ndi nsembe zophera, ndi nsembe zaufa, ndi zonunkhira, ndi kudza nazo zamiyamikiro, ku nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17

Onani Yeremiya 17:26 nkhani