Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 17:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu Yehova, ciyembekezo ca Israyeli, onse amene akukusiyani Inu adzakhala ndi manyazi; onse ondicokera Ine adzalembedwa m'dothi, cifukwa asiya Yehova, kasupe wa madzi amoyo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 17

Onani Yeremiya 17:13 nkhani