Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 16:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inu Yehova, mphamvu yanga, ndi linga langa, pothawirapo panga tsiku la msauko, amitundu adzadza kwa Inu kucokera ku malekezero a dziko lapansi, ndipo adzati, Makolo athu analandira colowa ca bodza lokha, zopanda pace ndi zinthu zosapindula nazo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 16

Onani Yeremiya 16:19 nkhani