Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 14:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi mwakanadi Yuda? kodi mtima wanu wanyansidwa ndi Ziyoni? bwanji mwatipanda ife, ndipo tiribe kucira? Tinayembekeza mtendere, koma sizinafike zabwino; tinayembekeza nthawi yakucira, ndipo taonani mantha!

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 14

Onani Yeremiya 14:19 nkhani