Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 14:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu amene adzanenera kwa inu adzaponyedwa kunja m'miseu ya Yerusalemu cifukwa ca cirala ndi lupanga; ndipo adzasowa akuwaika, ndi akazi ao, ndi ana ao amuna ndi akazi; ndipo ndidzatsanulira pa iwo zoipa zao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 14

Onani Yeremiya 14:16 nkhani