Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 14:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa ine, Aneneri anenera zonama m'dzina langa; sindinatuma iwo, sindinauza iwo, sindinanena nao; anenera kwa inu masomphenya onama, ndi ula, ndi cinthu cacabe, ndi cinyengo ca mtima wao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 14

Onani Yeremiya 14:14 nkhani