Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 14:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene asala cakudya, sindidzamva kupfuula kwao; ndipo pamene apereka nsembe yopsereza, ndi nsembe yaufa sindidzawalandira; koma ndidzawatha ndi lupanga, ndi cirala, ndi caola.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 14

Onani Yeremiya 14:12 nkhani