Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 13:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lemekezani Yehova Mulungu wanu, kusanade, mapazi anu asanakhumudwe pa mapiri acizirezire; nimusanayembekeze kuunika, Ive asanasandutse kuunikaku mthunzi wa imfa, ndi kukuyesa mdima wa bii.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 13

Onani Yeremiya 13:16 nkhani