Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 13:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Atero Yehova kwa ine, Pita, udzigulire mpango wabafuta, nudzimangire m'cuuno mwako, usauike m'madzi.

2. Ndipo ndinagula mpango monga mwa mau a Yehova, ndi kubvala m'cuuno mwanga.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 13