Akufunkha afika pa mapiri oti se m'cipululu; pakuti lupanga la Yehova lilusa kuyambira pa mbali yina ya dziko kufikira ku mbali yina; palibe thupi lokhala ndi mtendere.