Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 11:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ine ndinanga mwana wa nkhosa wofatsa wotengedwa kukaphedwa; ndipo sindinadziwa kuti anandicitira ine ciwembu, kuti, Tiononge mtengo ndi zipatso zace, timdule iye pa dziko la amoyo, kuti dzina lace lisakumbukikenso.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 11

Onani Yeremiya 11:19 nkhani