Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 11:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abwerera kucitanso zoipa za makolo ao, amene anakana kumva mau anga; ndipo atsata milungu yina kuti aitumikire; nyumba ya Israyeli ndi nyumba ya Yuda zaswa pangano langa limene ndinapangana ndi makolo ao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 11

Onani Yeremiya 11:10 nkhani