Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 10:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wosaopa Inu ndani, Mfumu ya amitundu? pakuti kukuopani ndi kwanu; pakuti mwa anzeru onse a amitundu, ndi m'maufumu ao onse, mulibe akunga Inu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 10

Onani Yeremiya 10:7 nkhani