Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 10:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti abusa apulukira, sanafunsire kwa Yehova; cifukwa cace sanapindula; zoweta zao zonse zabalalika.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 10

Onani Yeremiya 10:21 nkhani