Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 10:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Tamvani mau amene Yehova anena kwa inu, nyumba ya Israyeli;

2. atero Yehova, a Musaphunzire njira ya amitundu, musaope zizindikiro za m'thambo; pakuti amitundu aziopa izo.

3. Pakuti miyambo ya anthu iri yacabe, pakuti wina adula mtengo m'nkhalango, nchito ya manja a mmisiri ndinkhwangwa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 10