Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 1:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova anati kwa ine, Usati, ndine mwana pakuti udzanka kwa yense amene ndidzakutumako iwe, nudzanena conse cimene ndidzakuuza.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 1

Onani Yeremiya 1:7 nkhani