Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anamdzeranso masiku a Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, kufikira Zedekiya mwana wace wa Yosiya mfumu ya Yuda atatsiriza zaka khumi ndi cimodzi; kufikira a ku Yerusalemu anatengedwa ndende mwezi wacisanu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 1

Onani Yeremiya 1:3 nkhani