Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 1:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa, taona, ndakuyesa iwe lero mudzi walinga, mzati wacitsulo, makoma amkuwa, pa dziko lonse, ndi pa mafumu a Yuda, ndi pa akuru ace, ndi pa ansembe ace, ndi pa anthu a m'dziko.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 1

Onani Yeremiya 1:18 nkhani