Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti, taona, ndidzaitana mabanja onse a maufumu a kumpoto, ati Yehova; ndipo adzafika nadzaika yense mpando wacifumu wace pa zipata za Yerusalemu, ndi pa malinga onse ozinga pamenepo, ndi pa midzi yonse ya Yuda.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 1

Onani Yeremiya 1:15 nkhani