Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 4:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndati ndikuululira ici, ndi kuti, Ugule aka pamaso pa nzika, ndi pamaso pa akulu a anthu a kwathu. Ukafuna kuombola ombola; koma ukapanda kuombola, undiuze, ndidziwe; pakuti palibe woombola koma iwe, ndi ine pambuyo pako. Pamenepo anati, Ndidzaombola.

Werengani mutu wathunthu Rute 4

Onani Rute 4:4 nkhani