Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 4:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Boazi anatenga Rute, nakhala iye mkazi wace; ndipo analowa kwa iye; nalola Yehova kuti aime, ndipo anabala mwana wamwamuna.

Werengani mutu wathunthu Rute 4

Onani Rute 4:13 nkhani