Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pa nthawi ya kudya Boazi ananena naye, Sendera kuno, nudyeko mkate; nusunse nthongo yako m'vinyo wosasayo. Nakhala iye m'mbali mwa ocekawo; ndipo anamtambasulira dzanja kumninkha tirigu wokazinga, nadya iye, nakhuta, nasiyapo.

Werengani mutu wathunthu Rute 2

Onani Rute 2:14 nkhani