Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Rute 1:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ananyamuka iyeyu ndi apongozi ace kuti abwerere kucoka m'dziko la Moabu; pakuti adamva m'dziko la Moabu kuti Yehova adasamalira anthu ace ndi kuwapatsa cakudya.

Werengani mutu wathunthu Rute 1

Onani Rute 1:6 nkhani