Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 9:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuka ku nyumba ya atate wace ku Ofira, nawapha abale ace ana a Yerubaala, ndiwo amuna makumi asanu ndi awiri, pa thanthwe limodzi; koma Yotamu mwana wamng'ono wa Yerubaala anatsalako; pakuti anabisala.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:5 nkhani