Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 9:48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Abimeleki anakwera kumka ku phiri la Zalimoni, iye ndi anthu onse anali naye; natenga nkhwangwa m'dzanja lace Abimeleki, nadula nthambi kumitengo, nainyamula ndi kulika paphewa pace, nati kwa anthu okhala naye, Ici munaciona ndacita, fulumirani, mucite momwemo.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:48 nkhani