Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 9:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwenzi anthu awa akadakhala m'dzanja langa; ndikadamcotsadi Abimeleki. Ndipo anati kwa Abimeleki, Curukitsa khamu lako, nuturuke.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:29 nkhani