Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 9:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nenanitu m'makutu mwa eni ace onse a ku Sekemu, Cokomera inu nciti, akulamulireni ana amuna onse a Yerubaala ndiwo amuna makumi asanu ndi awiri, kapena akulamulireni mwamuna mmodzi? mukumbukilenso kuti ine ndine wa pfuko lanu ndi nyama yanu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:2 nkhani