Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 5:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Kodi sanapeza, sanagawa zofunkha?Namwali, anamwali awiri kwa munthu ali yense.Cofunkha ca nsaru za mawanga mawanga kwa Sisera;Cofunkha ca nsaru za mawanga mawanga, za maluwa,Nsaru za mawanga mawanga, za maluwa konse konse, kwa cofunkha ca khosi lace.

31. Adani anu onse, Yehova, atayike momwemo.Koma iwo akukonda Inu akhale ngati dzuwa loturuka mu mphamvu yace.Ndipo dziko linapumula zaka makumi anai.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 5