Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 4:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Israyeli anapfuula kwa Yehova; pakuti anali nao magareta acitsulo mazana asanu ndi anai; napsinja ana a Israyeli kolimba zaka makumi awiri.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 4

Onani Oweruza 4:3 nkhani