Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 3:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene ana a Israyeli anapfuula kwa Yehova, Yehova anawaukitsira mpulumutsi, Ehudi mwana wa Gera, Mbenjamini, munthu wamanzere, ndipo ana a Israyeli anatumiza mtulo m'dzanja lace Ikwa Egiloni mfumu ya Moabu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 3

Onani Oweruza 3:15 nkhani