Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 16:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anasonkhana akalonga a Afilisti kuperekera Dagoni mulungu wao nsembe yaikuru, ndi kusekerera; pakuti anati, Mulungu wathu wapereka Samsoni mdani wathu m'dzanja lathu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 16

Onani Oweruza 16:23 nkhani